---
Translated Materials for the Day of Prayer for the Peace of Jerusalem
Zinthu zomwe mungangwirise ntchito
Tools and Resources
Pa musipa pali mabuku ndi zinthu zambiri mungangwirise nchito pochukisa tsiku lopempherera mtendere wa Yerusalemu kundera lanu.
Below are several tools and resources you can use to promote the Day of Prayer for the Peace of Jerusalem in your region.
Bana
Flyer
Bana ndichikalata chomwe pali masomphenya, mndanda wa tsongolere ndi mautumiki, mbali yomwe mungatengepo ndizolinga zachaka chino.
The flyer is a general information piece that includes a description of the vision, a list of participating leaders and ministries, suggestions on how you can be involved, and our goals for this year.
-- Bana (PDF)--
-- Flyer (PDF)--